Law Commission conducts Public Awareness of the Laws with Accountant General

Ife a Law Commission tinali ku ofesi ya Accountant General. Lero ndi tsiku lachiwiri ku ofesiyi; kuunikira ogwira ntchito za Lamulo lokhudza Ukwati, Kutha kwa Ukwati komanso Ubale wa Banja komanso Lamulo Loyendetsera Katundu Wamasiye (Kalata Losonyeza Mayina a Anthu Oyenera Kulandira Chuma Chamasiye, Kutenga Katundu ndi Chitetezo)
Mmusimu muona zithunzi za mmene zinaliri lero

Similar Posts

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *