Law Commission conducts Public Awareness of the Laws with Accountant General
Ife a Law Commission tinali ku ofesi ya Accountant General. Lero ndi tsiku lachiwiri ku ofesiyi; kuunikira ogwira ntchito za Lamulo lokhudza Ukwati, Kutha kwa Ukwati komanso Ubale wa Banja komanso Lamulo Loyendetsera Katundu Wamasiye (Kalata Losonyeza Mayina a Anthu Oyenera Kulandira Chuma Chamasiye, Kutenga Katundu ndi Chitetezo) Mmusimu muona zithunzi za mmene zinaliri lero
